Deuteronomo 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iweyo pita pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena. Iweyo ndiye udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzakuuza,+ ndipo tidzamvera ndi kuchita zomwezo.’ Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+
27 Iweyo pita pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena. Iweyo ndiye udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzakuuza,+ ndipo tidzamvera ndi kuchita zomwezo.’
28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+