2 Mafumu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atalowa mumzindawo, anapeza akuluakulu a asilikali atakhalakhala. Kenako iye anati: “Ndili nanu mawu inu+ mkulu wa asilikali.” Ndiyeno Yehu anati: “Ndani kwenikweni pakati pa tonsefe?” Iye anayankha kuti: “Inuyo mkulu wa asilikali.”
5 Atalowa mumzindawo, anapeza akuluakulu a asilikali atakhalakhala. Kenako iye anati: “Ndili nanu mawu inu+ mkulu wa asilikali.” Ndiyeno Yehu anati: “Ndani kwenikweni pakati pa tonsefe?” Iye anayankha kuti: “Inuyo mkulu wa asilikali.”