Genesis 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulamu atamva zimenezi anati: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo amene adzakhale wolowa nyumba yanga ndi munthu wa ku Damasiko, Eliezere.”+ Genesis 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Rakele ataona kuti sanaberekere Yakobo mwana, anayamba kuchitira nsanje m’bale wake. Iye anauza Yakobo+ kuti: “Mundipatse ana, apo ayi kuli bwino ndingofa.”+
2 Abulamu atamva zimenezi anati: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo amene adzakhale wolowa nyumba yanga ndi munthu wa ku Damasiko, Eliezere.”+
30 Ndiyeno Rakele ataona kuti sanaberekere Yakobo mwana, anayamba kuchitira nsanje m’bale wake. Iye anauza Yakobo+ kuti: “Mundipatse ana, apo ayi kuli bwino ndingofa.”+