Ezekieli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri amene ali pakati pawo adzanyamula katundu wake paphewa n’kumapita mu mdima. Adzaboola khoma n’kutulukirapo.+ Iye adzaphimba kumaso kuti asaone dziko.
12 Mtsogoleri amene ali pakati pawo adzanyamula katundu wake paphewa n’kumapita mu mdima. Adzaboola khoma n’kutulukirapo.+ Iye adzaphimba kumaso kuti asaone dziko.