Yohane 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho alongo akewo anatumiza uthenga kwa Yesu, kuti: “Ambuye! amene mumamukonda+ uja akudwala.” Machitidwe 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Popeza kuti Luda anali pafupi ndi Yopa,+ ophunzirawo atamva kuti Petulo ali mumzinda umenewu, anatumiza amuna awiri kukamudandaulira kuti: “Chonde mufike kwathuku msanga.”
38 Popeza kuti Luda anali pafupi ndi Yopa,+ ophunzirawo atamva kuti Petulo ali mumzinda umenewu, anatumiza amuna awiri kukamudandaulira kuti: “Chonde mufike kwathuku msanga.”