Mateyu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.” Mateyu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+ Luka 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiponso, munali akhate ambiri mu Isiraeli m’nthawi ya mneneri Elisa. Komabe palibe aliyense wa iwo amene anayeretsedwa, koma Namani, mwamuna wa ku Siriya.”+
2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”
5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+
27 Ndiponso, munali akhate ambiri mu Isiraeli m’nthawi ya mneneri Elisa. Komabe palibe aliyense wa iwo amene anayeretsedwa, koma Namani, mwamuna wa ku Siriya.”+