Maliko 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wogontha komanso wovutika kulankhula. Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.+ Luka 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho poyankha anauza amuna awiri aja kuti: “Pitani+ mukamuuze Yohane zimene mwaona ndi kumva: Akhungu+ akuona, olumala akuyenda, akhate akuyeretsedwa, ogontha akumva, akufa akuukitsidwa ndipo aumphawi akumva+ uthenga wabwino.+
32 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wogontha komanso wovutika kulankhula. Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.+
22 Choncho poyankha anauza amuna awiri aja kuti: “Pitani+ mukamuuze Yohane zimene mwaona ndi kumva: Akhungu+ akuona, olumala akuyenda, akhate akuyeretsedwa, ogontha akumva, akufa akuukitsidwa ndipo aumphawi akumva+ uthenga wabwino.+