2 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene Asiriya a ku Damasiko+ anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.+ Machitidwe 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa.
5 Pamene Asiriya a ku Damasiko+ anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.+
2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa.