Miyambo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu amene amakwiya msanga amachita zinthu zopusa,+ koma munthu wotha kuganiza bwino amadedwa.+ Mlaliki 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usamafulumire kukwiya mumtima mwako,+ pakuti anthu opusa ndi amene sachedwa kupsa mtima.+