2 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Elisa anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene ndimam’tumikira,+ sindilandira.”+ Ndiyeno Namani anayamba kum’kakamiza kuti alandire, koma iye anakanabe.
16 Koma Elisa anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene ndimam’tumikira,+ sindilandira.”+ Ndiyeno Namani anayamba kum’kakamiza kuti alandire, koma iye anakanabe.