Mateyu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+ Yohane 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iye ponena izi sikuti anali kudera nkhawa osauka ayi, koma chifukwa anali wakuba.+ Iye anali wosunga bokosi la ndalama,+ ndipo anali kutengamo ndalama zimene zinali kuponyedwa m’bokosilo. Machitidwe 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Sindinasirire mwa nsanje siliva, golide kapena chovala cha munthu.+
8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+
6 Koma iye ponena izi sikuti anali kudera nkhawa osauka ayi, koma chifukwa anali wakuba.+ Iye anali wosunga bokosi la ndalama,+ ndipo anali kutengamo ndalama zimene zinali kuponyedwa m’bokosilo.