Ekisodo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yehova anamuuzanso kuti: “Lowetsa dzanja lako m’malaya pachifuwa.” Choncho Mose analowetsa dzanja lake m’malaya. Koma politulutsa, dzanja lakelo linali litachita khate, ndipo linaoneka loyera kwambiri ngati chipale chofewa.+ Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+ Miyambo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+
6 Kenako Yehova anamuuzanso kuti: “Lowetsa dzanja lako m’malaya pachifuwa.” Choncho Mose analowetsa dzanja lake m’malaya. Koma politulutsa, dzanja lakelo linali litachita khate, ndipo linaoneka loyera kwambiri ngati chipale chofewa.+
10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+
6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+