Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 18:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako mlonda uja anaonanso munthu wina akuthamanga. Ndiyeno mlondayo anaitana mlonda wa pachipata ndi kumuuza kuti: “Taona! Munthu winanso akuthamanga ali yekha.” Pamenepo mfumu inati: “Ameneyunso akubweretsa uthenga.”

  • Salimo 127:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+

      Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+

      Yehova akapanda kulondera mzinda,+

      Alonda amakhala maso pachabe.+

  • Maliko 13:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Zili ngati munthu amene anali kupita kutali kudziko lina,+ amene anasiya nyumba m’manja mwa akapolo ake, aliyense pa ntchito yake, ndi kulamula mlonda wa pachipata kuti azikhala maso.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena