Yeremiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+ Luka 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano atayandikira mzinda wa Yerusalemu, anaona mzindawo n’kuyamba kuulirira.+ Machitidwe 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndinali kutumikira+ Ambuye monga kapolo, modzichepetsa kwambiri,+ ndi misozi komanso ndi mayesero amene anandigwera chifukwa cha ziwembu+ za Ayuda.
9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+
19 Ndinali kutumikira+ Ambuye monga kapolo, modzichepetsa kwambiri,+ ndi misozi komanso ndi mayesero amene anandigwera chifukwa cha ziwembu+ za Ayuda.