1 Akorinto 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu. 1 Atesalonika 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinali kungodzifunira ulemerero kwa anthu+ ayi, kaya kwa inu kapena kwa anthu ena. Sitinatero, ngakhale kuti monga atumwi a Khristu, tikanatha kupempha kuti mutilipirire+ zinthu zina kuti mutithandize. 1 Petulo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Osati mochita ufumu+ pa anthu amene ali cholowa chochokera kwa Mulungu,+ koma mukhale zitsanzo kwa gulu la nkhosa.+
9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu.
6 Sitinali kungodzifunira ulemerero kwa anthu+ ayi, kaya kwa inu kapena kwa anthu ena. Sitinatero, ngakhale kuti monga atumwi a Khristu, tikanatha kupempha kuti mutilipirire+ zinthu zina kuti mutithandize.
3 Osati mochita ufumu+ pa anthu amene ali cholowa chochokera kwa Mulungu,+ koma mukhale zitsanzo kwa gulu la nkhosa.+