-
2 Samueli 18:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kenako mlonda uja anaonanso munthu wina akuthamanga. Ndiyeno mlondayo anaitana mlonda wa pachipata ndi kumuuza kuti: “Taona! Munthu winanso akuthamanga ali yekha.” Pamenepo mfumu inati: “Ameneyunso akubweretsa uthenga.”
-