Oweruza 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Aisiraeli anasautsika kwadzaoneni chifukwa cha Amidiyani. Pamenepo, ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Oweruza 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani+ inu Mulungu wathu, chifukwa takusiyani ndipo tikutumikira Abaala.”+ 2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+ Salimo 78:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+
6 Choncho Aisiraeli anasautsika kwadzaoneni chifukwa cha Amidiyani. Pamenepo, ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+
10 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani+ inu Mulungu wathu, chifukwa takusiyani ndipo tikutumikira Abaala.”+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+
34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+