2 Mafumu 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehoahazi anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda motsatira tchimo la Yerobowamu+ mwana wa Nebati, limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+ Iye sanapatuke pa tchimolo. Hoseya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Efuraimu waponderezedwa. Akusautsidwa moyenereradi,+ chifukwa anatsatira dala mdani wake.+
2 Yehoahazi anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda motsatira tchimo la Yerobowamu+ mwana wa Nebati, limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+ Iye sanapatuke pa tchimolo.