2 Mafumu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wa Mulungu woonayo+ anakwiyira mfumuyo kwambiri, ndipo anati: “Mukanalasa maulendo asanu kapena maulendo 6! Mukanatero mukanaphadi Asiriya mpaka kuwamaliza, koma tsopano mudzawagonjetsa katatu kokha.”+
19 Munthu wa Mulungu woonayo+ anakwiyira mfumuyo kwambiri, ndipo anati: “Mukanalasa maulendo asanu kapena maulendo 6! Mukanatero mukanaphadi Asiriya mpaka kuwamaliza, koma tsopano mudzawagonjetsa katatu kokha.”+