2 Mafumu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma sanapange mabeseni asiliva, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ malipenga,+ ndi ziwiya zilizonse zagolide kapena zasiliva za m’nyumba ya Yehova kuchokera pa ndalama zimene anthu anali kubweretsa kunyumba ya Yehova,+
13 Koma sanapange mabeseni asiliva, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ malipenga,+ ndi ziwiya zilizonse zagolide kapena zasiliva za m’nyumba ya Yehova kuchokera pa ndalama zimene anthu anali kubweretsa kunyumba ya Yehova,+