19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, momwe anamenyera nkhondo+ ndi momwe analamulirira, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
12 Nkhani zina zokhudza Yehoasi ndi zonse zimene anachita ndiponso zochita zake zamphamvu, komanso momwe anamenyanirana+ ndi Amaziya mfumu ya Yuda, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.