Levitiko 13:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Masiku onse pamene akudwala nthendayo azikhala wodetsedwa. Iye ndi wodetsedwa ndipo azikhala payekha. Azikhala kunja kwa msasa.+ Deuteronomo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Samalani ndi mliri wa khate+ ndi kuonetsetsa kuti mukuchita zonse zimene ansembe achilevi adzakulangizani.+ Muzichita mosamala zonse zimene ndawalamula.+
46 Masiku onse pamene akudwala nthendayo azikhala wodetsedwa. Iye ndi wodetsedwa ndipo azikhala payekha. Azikhala kunja kwa msasa.+
8 “Samalani ndi mliri wa khate+ ndi kuonetsetsa kuti mukuchita zonse zimene ansembe achilevi adzakulangizani.+ Muzichita mosamala zonse zimene ndawalamula.+