2 “Munthu akatuluka zotupa, kapena nkhanambo,+ kapena chikanga pakhungu lake, ndipo chasintha n’kukhala nthenda ya khate,+ azibwera naye kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake amenenso ndi ansembe.+
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+