1 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.” 1 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+ Salimo 72:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+
5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”
9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+
72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+