1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda. 2 Mbiri 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nkhani zina zokhudza Uziya,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda.
22 Nkhani zina zokhudza Uziya,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+