2 Mafumu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhani zina zokhudza Azariya ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
6 Nkhani zina zokhudza Azariya ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.