2 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pomalizira pake, Yerobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake, mafumu a Isiraeli, ndipo Zekariya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
29 Pomalizira pake, Yerobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake, mafumu a Isiraeli, ndipo Zekariya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.