24 Kuwonjezera apo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya+ za m’nyumba ya Mulungu woona+ n’kuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko+ za nyumba ya Yehova. Kenako anakadzimangira maguwa ansembe m’makona onse a mu Yerusalemu.+
19 Ziwiya zonse+ zimene Mfumu Ahazi+ anasiya kuzigwiritsira ntchito mu ulamuliro wake chifukwa cha kusakhulupirika kwake,+ tazikonza ndi kuziyeretsa+ ndipo zili pafupi ndi guwa lansembe la Yehova.”