Deuteronomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule+ mizati yawo yopatulika+ ndi kutentha zifaniziro zawo zogoba.+ Deuteronomo 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Usabzale mtengo wa mtundu uliwonse kuti ukhale mzati woti uziulambira pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wako limene udzadzipangira.+ Mika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzazula mizati yanu yopatulika+ imene ili pakati panu ndi kuwononga mizinda yanu.
5 “Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule+ mizati yawo yopatulika+ ndi kutentha zifaniziro zawo zogoba.+
21 “Usabzale mtengo wa mtundu uliwonse kuti ukhale mzati woti uziulambira pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wako limene udzadzipangira.+