Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Genesis 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakhazikitsa pangano langa pakati pa ine ndi iwe,+ pangano lakuti ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zako.”+
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+
2 Ndidzakhazikitsa pangano langa pakati pa ine ndi iwe,+ pangano lakuti ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zako.”+