Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+ Yesaya 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova, Wokuwombola+ ndiponso amene anakuumba kuyambira uli m’mimba, wanena kuti: “Ine Yehova ndachita zonse. Ndinatambasula ndekha kumwamba,+ ndi kukhazikitsa dziko lapansi.+ Kodi ndani anali nane?
24 Yehova, Wokuwombola+ ndiponso amene anakuumba kuyambira uli m’mimba, wanena kuti: “Ine Yehova ndachita zonse. Ndinatambasula ndekha kumwamba,+ ndi kukhazikitsa dziko lapansi.+ Kodi ndani anali nane?