Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Genesis 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Motero, kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse za mmenemo zinamalizidwa kulengedwa.+ Yobu 38:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi unali kuti pamene ndinkaika maziko a dziko lapansi?+Ndiuze ngati uli womvetsa zinthu. Yesaya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+ ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndimafuulira maziko a dziko lapansi ndi kumwamba, kuti ziimirire.+ Zekariya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uthenga wokhudza Isiraeli: “Awa ndi mawu a Yehova okhudza Isiraeli.” Yehova, amene anatambasula miyamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi+ komanso kupanga mzimu+ n’kuuika mwa munthu, wanena kuti:
13 Komanso dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+ ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndimafuulira maziko a dziko lapansi ndi kumwamba, kuti ziimirire.+
12 Uthenga wokhudza Isiraeli: “Awa ndi mawu a Yehova okhudza Isiraeli.” Yehova, amene anatambasula miyamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi+ komanso kupanga mzimu+ n’kuuika mwa munthu, wanena kuti: