2 Samueli 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+ 2 Samueli 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wa Isiraeli analankhula,Thanthwe la Isiraeli linandiuza kuti,+‘Munthu wolamulira anthu akakhala wolungama,+N’kumalamulira moopa Mulungu,+ Salimo 78:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Iye anayamba kuwaweta malinga ndi mtima wake wosagawanika,+Ndipo anayamba kuwatsogolera mwaluso.+
15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+
3 Mulungu wa Isiraeli analankhula,Thanthwe la Isiraeli linandiuza kuti,+‘Munthu wolamulira anthu akakhala wolungama,+N’kumalamulira moopa Mulungu,+ Salimo 78:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Iye anayamba kuwaweta malinga ndi mtima wake wosagawanika,+Ndipo anayamba kuwatsogolera mwaluso.+