31 Davide anatulutsa anthu amene anali mumzindawo kuti akawagwiritse ntchito yocheka miyala, kusula zitsulo zakuthwa,+ nkhwangwa zachitsulo ndi kuumba njerwa. Zimenezi n’zimene anachitira mizinda yonse ya ana a Amoni. Pamapeto pake, Davide pamodzi ndi anthu onse anabwerera ku Yerusalemu.