Miyambo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amam’konda,+ monga momwe bambo amadzudzulira mwana amene amakondwera naye.+
12 chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amam’konda,+ monga momwe bambo amadzudzulira mwana amene amakondwera naye.+