Deuteronomo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu anali kukuwongolerani, ngati mmene bambo amawongolerera mwana wake.+ Miyambo 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwana wanga, mtima wako ukakhala wanzeru,+ ndithu mtima wanga udzasangalala.+ Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+ Aheberi 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiponso, bambo athu otibereka, amene anali ndi thupi lanyama ngati lathuli anali kutilanga,+ ndipo tinali kuwalemekeza. Kuli bwanji ndi Atate wa moyo wathu wauzimu. Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+
5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu anali kukuwongolerani, ngati mmene bambo amawongolerera mwana wake.+
7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+
9 Ndiponso, bambo athu otibereka, amene anali ndi thupi lanyama ngati lathuli anali kutilanga,+ ndipo tinali kuwalemekeza. Kuli bwanji ndi Atate wa moyo wathu wauzimu. Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+