2 Samueli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno pamene mfumu inali kukhala m’nyumba yake,+ ndipo Yehova ataipatsa mpumulo kwa adani ake onse oizungulira,+ 1 Mbiri 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu?+ Kodi sanakupatseni mpumulo m’dziko lonseli?+ Pakuti iye wapereka m’manja mwanga anthu a m’dzikoli, ndipo dzikoli lagonjetsedwa pamaso pa Yehova+ ndi pa anthu ake.
7 Ndiyeno pamene mfumu inali kukhala m’nyumba yake,+ ndipo Yehova ataipatsa mpumulo kwa adani ake onse oizungulira,+
18 “Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu?+ Kodi sanakupatseni mpumulo m’dziko lonseli?+ Pakuti iye wapereka m’manja mwanga anthu a m’dzikoli, ndipo dzikoli lagonjetsedwa pamaso pa Yehova+ ndi pa anthu ake.