2 Samueli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno pamene mfumu inali kukhala m’nyumba yake,+ ndipo Yehova ataipatsa mpumulo kwa adani ake onse oizungulira,+ Miyambo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+
7 Ndiyeno pamene mfumu inali kukhala m’nyumba yake,+ ndipo Yehova ataipatsa mpumulo kwa adani ake onse oizungulira,+
7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+