1 Mafumu 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Elihorefi ndi Ahiya, ana a Sisa, omwe anali alembi,+ ndi wolemba zochitika dzina lake Yehosafati,+ mwana wa Ahiludi. 2 Mbiri 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 anali kuyang’anira+ anthu onyamula katundu+ ndi anthu onse ogwira ntchito zosiyanasiyana. Panalinso Alevi+ amene anali alembi,+ akapitawo, ndi alonda a pazipata.+
3 Elihorefi ndi Ahiya, ana a Sisa, omwe anali alembi,+ ndi wolemba zochitika dzina lake Yehosafati,+ mwana wa Ahiludi.
13 anali kuyang’anira+ anthu onyamula katundu+ ndi anthu onse ogwira ntchito zosiyanasiyana. Panalinso Alevi+ amene anali alembi,+ akapitawo, ndi alonda a pazipata.+