1 Mbiri 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Eliezere, mtsogoleri wawo anali Rehabiya.+ Eliezere sanakhalenso ndi ana ena aamuna, koma Rehabiya anali ndi ana ochuluka kwambiri.
17 Ana a Eliezere, mtsogoleri wawo anali Rehabiya.+ Eliezere sanakhalenso ndi ana ena aamuna, koma Rehabiya anali ndi ana ochuluka kwambiri.