1 Mbiri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Heburoni anali Yeriya amene anali mtsogoleri wawo, wachiwiri wake anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli, ndipo wachinayi anali Yekameamu.+
19 Ana a Heburoni anali Yeriya amene anali mtsogoleri wawo, wachiwiri wake anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli, ndipo wachinayi anali Yekameamu.+