1 Mbiri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mfumu Davide inauza Orinani kuti: “Iyayi, ineyo ndigula ndipo ndipereka ndalama zake zonse,+ chifukwa sindingatenge zinthu zako n’kupita nazo kwa Yehova kukapereka nsembe zopsereza popanda kulipira.” Miyambo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+ ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.+
24 Koma Mfumu Davide inauza Orinani kuti: “Iyayi, ineyo ndigula ndipo ndipereka ndalama zake zonse,+ chifukwa sindingatenge zinthu zako n’kupita nazo kwa Yehova kukapereka nsembe zopsereza popanda kulipira.”
9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+ ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.+