Yobu 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sangazigule ndi golide wa ku Ofiri,+Kapena mwala wosowa wa onekisi ndi wa safiro.