Yesaya 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachititsa kuti anthu azisowa kwambiri kuposa golide woyengedwa bwino,+ ndiponso ndidzachititsa kuti anthu ochokera kufumbi azisowa kwambiri kuposa golide wa ku Ofiri.+
12 Ndidzachititsa kuti anthu azisowa kwambiri kuposa golide woyengedwa bwino,+ ndiponso ndidzachititsa kuti anthu ochokera kufumbi azisowa kwambiri kuposa golide wa ku Ofiri.+