Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:61
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.”

  • 2 Mafumu 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+

  • Maliko 12:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, maganizo ako onse ndi mphamvu zako zonse.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena