Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Chilamulocho ndicho maumboni,*+ malangizo+ ndi zigamulo+ zimene Mose anauza ana a Isiraeli pamene anatuluka mu Iguputo.

  • Deuteronomo 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Muzionetsetsa kuti mukusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ maumboni ake+ ndi zigamulo+ zake zimene wakupatsani.+

  • Deuteronomo 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Uzisunga malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene ndikukupatsa lero, mwa kuzitsatira.+

  • Deuteronomo 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+

  • 1 Mafumu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uzimvera Yehova Mulungu wako mwa kuyenda m’njira zake,+ kusunga malamulo ake, zigamulo zake,+ ndi maumboni* ake, malinga ndi zimene zinalembedwa m’chilamulo cha Mose.+ Uzitero kuti udzakhale wanzeru m’zochita zako zonse, ndiponso kulikonse kumene udzapite.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena