Genesis 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+ 1 Samueli 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Davide anamufunsa kuti: “Uli mbali ya ndani, ndipo kwanu n’kuti?” Mwamunayo anayankha kuti: “Ndine Mwiguputo, kapolo wa Mwamaleki, koma mbuyanga anandisiya pano masiku atatu apitawa chifukwa cha kudwala.+
16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+
13 Ndiyeno Davide anamufunsa kuti: “Uli mbali ya ndani, ndipo kwanu n’kuti?” Mwamunayo anayankha kuti: “Ndine Mwiguputo, kapolo wa Mwamaleki, koma mbuyanga anandisiya pano masiku atatu apitawa chifukwa cha kudwala.+