Genesis 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaberekanso mwana wina wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Shela. Mwana ameneyu anam’bereka ali ku Akizibu. + Numeri 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho ana aamuna a Yuda mwa mabanja awo anali awa: Shela+ amene anali kholo la banja la Ashela, Perezi+ amene anali kholo la banja la Aperezi, ndi Zera+ amene anali kholo la banja la Azera.
5 Anaberekanso mwana wina wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Shela. Mwana ameneyu anam’bereka ali ku Akizibu. +
20 Choncho ana aamuna a Yuda mwa mabanja awo anali awa: Shela+ amene anali kholo la banja la Ashela, Perezi+ amene anali kholo la banja la Aperezi, ndi Zera+ amene anali kholo la banja la Azera.