1 Mbiri 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’masiku a Sauli, iwo anachita nkhondo ndi Ahagara+ n’kuwagonjetsa. Kenako anayamba kukhala m’mahema awo m’dera lonse lakum’mawa kwa Giliyadi. Salimo 83:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amenewa ndi anthu okhala m’mahema a Edomu+ ndi m’mahema a Isimaeli, Amowabu+ ndi Ahagara,+
10 M’masiku a Sauli, iwo anachita nkhondo ndi Ahagara+ n’kuwagonjetsa. Kenako anayamba kukhala m’mahema awo m’dera lonse lakum’mawa kwa Giliyadi.