Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ng’ombeyo azichita nayo ngati mmene amachitira ndi ng’ombe ya nsembe yamachimo ija. Azichita momwemo. Ndipo wansembe aziwaphimbira machimo+ awo kuti akhululukidwe.

  • Levitiko 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo.

  • Numeri 15:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo wansembe azipereka nsembe yophimba machimo+ a khamu lonse la ana a Isiraeli. Akatero, anthuwo azikhululukidwa cholakwacho chifukwa anachita mosazindikira,+ komanso chifukwa apereka nsembe yopsereza kwa Yehova, ndiponso nsembe yamachimo kwa Yehova pa cholakwa chawocho.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena